-
Ekisodo 39:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Ndipo analowetsa zingwe ziwirizo pa zoikamo miyala ziwiri. Kenako anaika zoikamo miyala ziwirizo pansalu zamʼmapewa za efodi chakutsogolo.
-