Ekisodo 39:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Atatero anapanga mphete ziwiri zagolide nʼkuziika mʼmakona awiri a chovala pachifuwa kumbali yamkati yokhudzana ndi efodi.+
19 Atatero anapanga mphete ziwiri zagolide nʼkuziika mʼmakona awiri a chovala pachifuwa kumbali yamkati yokhudzana ndi efodi.+