Ekisodo 39:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndiyeno anapanga mphete zina ziwiri zagolide nʼkuziika kutsogolo kwa efodi, mʼmunsi mwa nsalu ziwiri zamʼmapewa, pafupi ndi polumikizira, pamwamba pa malo amene lamba* woluka walumikizana ndi efodi.
20 Ndiyeno anapanga mphete zina ziwiri zagolide nʼkuziika kutsogolo kwa efodi, mʼmunsi mwa nsalu ziwiri zamʼmapewa, pafupi ndi polumikizira, pamwamba pa malo amene lamba* woluka walumikizana ndi efodi.