-
Ekisodo 39:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Atatero anamanga chovala pachifuwacho ndi chingwe chabuluu. Chingwe chimenecho chinalowa mumphete za chovala pachifuwa komanso mphete za efodi. Zimenezi zinkathandiza kuti chovala pachifuwacho chisamasunthe koma chizikhala pamwamba pa lamba* woluka wa efodi, mogwirizana ndi zimene Yehova analamula Mose.
-