Ekisodo 39:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ndiyeno anapanga malaya odula manja ovala mkati mwa efodi. Anapangidwa ndi woomba nsalu ndipo anawapanga ndi ulusi wabuluu wokhawokha.+
22 Ndiyeno anapanga malaya odula manja ovala mkati mwa efodi. Anapangidwa ndi woomba nsalu ndipo anawapanga ndi ulusi wabuluu wokhawokha.+