-
Ekisodo 39:23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
23 Malaya odula manjawo anali otsegula pamwamba pake, pakatikati. Anali otsegula ngati chovala chakunkhondo cha mamba achitsulo. Potsegulapo panali popenderera mʼmphepete mwake kuti pasangʼambike.
-