Ekisodo 39:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Anaika belu kenako khangaza,* belu kenako khangaza, kuzungulira mpendero wamʼmunsi mwa malaya odula manja. Malayawo ankavala potumikira, mogwirizana ndi zimene Yehova analamula Mose.
26 Anaika belu kenako khangaza,* belu kenako khangaza, kuzungulira mpendero wamʼmunsi mwa malaya odula manja. Malayawo ankavala potumikira, mogwirizana ndi zimene Yehova analamula Mose.