Ekisodo 39:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Kenako anawomba nsalu ya ulusi wabwino kwambiri nʼkupangira mikanjo ya Aroni ndi ana ake.+