Ekisodo 39:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Anapanganso nduwira+ ya nsalu yabwino kwambiri, mipango yokongola yokulunga kumutu+ ya nsalu zabwino kwambiri ndi makabudula a nsalu*+ za ulusi wopota wabwino kwambiri.
28 Anapanganso nduwira+ ya nsalu yabwino kwambiri, mipango yokongola yokulunga kumutu+ ya nsalu zabwino kwambiri ndi makabudula a nsalu*+ za ulusi wopota wabwino kwambiri.