-
Ekisodo 39:31Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
31 Analowetsa chingwe chopangidwa ndi ulusi wabuluu mʼkachitsuloko kuti akamangirire panduwirayo, mogwirizana ndi zimene Yehova analamula Mose.
-