Ekisodo 39:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Choncho ntchito yonse ya chihema, kapena kuti chihema chokumanako, inatha ndipo Aisiraeli anachita zonse zimene Yehova analamula Mose.+ Anachitadi zomwezo. Ekisodo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 39:32 Nsanja ya Olonda,12/15/1995, ptsa. 12-13
32 Choncho ntchito yonse ya chihema, kapena kuti chihema chokumanako, inatha ndipo Aisiraeli anachita zonse zimene Yehova analamula Mose.+ Anachitadi zomwezo.