Ekisodo 40:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndipo udzaike beseni pakati pa chihema chokumanako ndi guwa lansembe nʼkuthiramo madzi.+