Levitiko 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Uza Aisiraeli* kuti, ‘Ngati munthu aliyense akufuna kupereka chiweto kwa Yehova kuti ikhale nsembe, azipereka ngʼombe, nkhosa kapena mbuzi.+
2 “Uza Aisiraeli* kuti, ‘Ngati munthu aliyense akufuna kupereka chiweto kwa Yehova kuti ikhale nsembe, azipereka ngʼombe, nkhosa kapena mbuzi.+