Levitiko 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kenako azipha ngʼombe yaingʼono pamaso pa Yehova. Ndiyeno ana a Aroni ansembe,+ azibweretsa magazi ake nʼkuwawaza mbali zonse za guwa lansembe,+ limene lili pakhomo la chihema chokumanako.
5 Kenako azipha ngʼombe yaingʼono pamaso pa Yehova. Ndiyeno ana a Aroni ansembe,+ azibweretsa magazi ake nʼkuwawaza mbali zonse za guwa lansembe,+ limene lili pakhomo la chihema chokumanako.