Levitiko 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ana a Aroni, ansembe, aziika moto paguwa lansembelo+ nʼkuyalapo nkhuni.