Levitiko 1:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma ngati akupereka mbalame kuti ikhale nsembe yake yopsereza yoperekedwa kwa Yehova, azipereka njiwa kapena ana a nkhunda.+
14 Koma ngati akupereka mbalame kuti ikhale nsembe yake yopsereza yoperekedwa kwa Yehova, azipereka njiwa kapena ana a nkhunda.+