Levitiko 1:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Wansembe azibweretsa mbalameyo paguwa lansembe nʼkudula* mutu wake. Akatero aziiwotcha paguwa lansembe kuti pakhale utsi, koma magazi ake aziwakhetsera pansi pambali pa guwa lansembelo.
15 Wansembe azibweretsa mbalameyo paguwa lansembe nʼkudula* mutu wake. Akatero aziiwotcha paguwa lansembe kuti pakhale utsi, koma magazi ake aziwakhetsera pansi pambali pa guwa lansembelo.