Levitiko 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ngati mukupereka nsembe yambewu yophika mʼchiwaya,+ izikhala ya ufa wabwino kwambiri wothira mafuta, yopanda zofufumitsa.
5 Ngati mukupereka nsembe yambewu yophika mʼchiwaya,+ izikhala ya ufa wabwino kwambiri wothira mafuta, yopanda zofufumitsa.