-
Levitiko 2:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Nsembe yambewu imene yapangidwa ndi zinthu zimenezi muzibwera nayo kwa Yehova. Muziipereka kwa wansembe ndipo iye azipita nayo paguwa lansembe.
-