Levitiko 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndipo zimene zatsala pansembe yambewu zizikhala za Aroni ndi ana ake, chifukwa ndi zopatulika koposa zochokera pansembe zowotcha pamoto+ zoperekedwa kwa Yehova.
10 Ndipo zimene zatsala pansembe yambewu zizikhala za Aroni ndi ana ake, chifukwa ndi zopatulika koposa zochokera pansembe zowotcha pamoto+ zoperekedwa kwa Yehova.