Levitiko 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “‘Ngati akupereka nsembe yamgwirizano*+ kwa Yehova ndipo akufuna kupereka ngʼombe yamphongo kapena yaikazi, azipereka yopanda chilema. Levitiko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:1 Nsanja ya Olonda,8/15/2000, ptsa. 15-16
3 “‘Ngati akupereka nsembe yamgwirizano*+ kwa Yehova ndipo akufuna kupereka ngʼombe yamphongo kapena yaikazi, azipereka yopanda chilema.