-
Levitiko 3:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Ndiyeno aziika dzanja lake pamutu pa ngʼombeyo ndipo iziphedwa pakhomo la chihema chokumanako. Akatero ana a Aroni ansembe, aziwaza magazi ake mbali zonse za guwa lansembe.
-