Levitiko 3:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndipo pambuziyo azitengapo mafuta okuta matumbo ndi mafuta onse amene ali pamatumbo,+ nʼkuwapereka kwa Yehova ngati nsembe yowotcha pamoto. Levitiko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:14 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),11/2019, tsa. 23
14 Ndipo pambuziyo azitengapo mafuta okuta matumbo ndi mafuta onse amene ali pamatumbo,+ nʼkuwapereka kwa Yehova ngati nsembe yowotcha pamoto.