Levitiko 3:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Wansembe aziwotcha zinthu zonsezi paguwa lansembe monga chakudya.* Imeneyi ndi nsembe yowotcha pamoto yakafungo kosangalatsa.* Mafuta onse ndi a Yehova.+ Levitiko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:16 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),11/2019, tsa. 23
16 Wansembe aziwotcha zinthu zonsezi paguwa lansembe monga chakudya.* Imeneyi ndi nsembe yowotcha pamoto yakafungo kosangalatsa.* Mafuta onse ndi a Yehova.+