Levitiko 4:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kenako azipaka ena mwa magaziwo panyanga za guwa lansembe+ limene lili pamaso pa Yehova, mʼchihema chokumanako. Magazi ena onse aziwathira pansi pa guwa lansembe zopsereza, limene lili pakhomo la chihema chokumanako.+
18 Kenako azipaka ena mwa magaziwo panyanga za guwa lansembe+ limene lili pamaso pa Yehova, mʼchihema chokumanako. Magazi ena onse aziwathira pansi pa guwa lansembe zopsereza, limene lili pakhomo la chihema chokumanako.+