Levitiko 4:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ngʼombeyo azichita nayo ngati mmene anachitira ndi ngʼombe ina ya nsembe yamachimo ija. Azichita zomwezo, ndipo wansembe aziwaphimbira machimo awo+ ndipo adzakhululukidwa.
20 Ngʼombeyo azichita nayo ngati mmene anachitira ndi ngʼombe ina ya nsembe yamachimo ija. Azichita zomwezo, ndipo wansembe aziwaphimbira machimo awo+ ndipo adzakhululukidwa.