-
Levitiko 4:35Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
35 Ndiyeno azichotsa mafuta onse a nkhosayo, monga mmene amachotsera mafuta a nkhosa yaingʼono yamphongo ya nsembe yamgwirizano. Akatero wansembe aziwotcha zinthu zimenezi paguwa lansembe pamwamba pa nsembe zowotcha pamoto zoperekedwa kwa Yehova.+ Wansembe aziphimba tchimo limene munthuyo wachita, ndipo adzakhululukidwa.’”+
-