Levitiko 5:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Munthu akakhudza chinthu chodetsedwa, kaya ikhale nyama yakufa yakuthengo, nyama yakufa yoweta kapena kamodzi mwa tizilombo topezeka tambiri,+ ngakhale kuti sanazindikire, iye ndi wodetsedwa ndipo wapalamula mlandu.
2 Munthu akakhudza chinthu chodetsedwa, kaya ikhale nyama yakufa yakuthengo, nyama yakufa yoweta kapena kamodzi mwa tizilombo topezeka tambiri,+ ngakhale kuti sanazindikire, iye ndi wodetsedwa ndipo wapalamula mlandu.