Levitiko 5:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kapenanso munthu akafulumira kulumbira kuti achita chinachake, kaya chabwino kapena choipa koma sanazindikire, kenako nʼkuzindikira kuti analumbira mofulumira, ndiye kuti wapalamula mlandu.*+
4 Kapenanso munthu akafulumira kulumbira kuti achita chinachake, kaya chabwino kapena choipa koma sanazindikire, kenako nʼkuzindikira kuti analumbira mofulumira, ndiye kuti wapalamula mlandu.*+