Levitiko 5:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Akapalamula mlandu wokhudzana ndi chimodzi mwa zinthu zimenezi, aziulula tchimo+ limene wachita.