Levitiko 5:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kenako azidontheza ena mwa magazi a nsembe yamachimo mʼmbali mwa guwa lansembe, koma magazi otsalawo aziwathira pansi pa guwa lansembelo.+ Imeneyi ndi nsembe yamachimo.
9 Kenako azidontheza ena mwa magazi a nsembe yamachimo mʼmbali mwa guwa lansembe, koma magazi otsalawo aziwathira pansi pa guwa lansembelo.+ Imeneyi ndi nsembe yamachimo.