Levitiko 5:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mbalame inayo aziipereka ngati nsembe yopsereza motsatira ndondomeko ya nthawi zonse.+ Choncho wansembe aziphimba machimo amene munthuyo wachita, ndipo adzakhululukidwa.+
10 Mbalame inayo aziipereka ngati nsembe yopsereza motsatira ndondomeko ya nthawi zonse.+ Choncho wansembe aziphimba machimo amene munthuyo wachita, ndipo adzakhululukidwa.+