Levitiko 5:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Wansembeyo aziphimba tchimo limene munthuyo wachita. Aziphimba tchimo lililonse mwa machimo amenewa ndipo adzakhululukidwa.+ Zinthu zimene zatsala pa nsembeyo zizikhala za wansembe+ mofanana ndi nsembe yambewu.’”+
13 Wansembeyo aziphimba tchimo limene munthuyo wachita. Aziphimba tchimo lililonse mwa machimo amenewa ndipo adzakhululukidwa.+ Zinthu zimene zatsala pa nsembeyo zizikhala za wansembe+ mofanana ndi nsembe yambewu.’”+