Levitiko 5:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Munthu akachimwa pochita chimodzi mwa zinthu zimene Yehova analamula kuti asachite, ngakhale kuti anachita mosazindikira, wapalamulabe mlandu ndipo aziyankha mlandu wa cholakwa chakecho.+
17 Munthu akachimwa pochita chimodzi mwa zinthu zimene Yehova analamula kuti asachite, ngakhale kuti anachita mosazindikira, wapalamulabe mlandu ndipo aziyankha mlandu wa cholakwa chakecho.+