Levitiko 6:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Mwamuna aliyense mwa ana a Aroni azidya mkatewo.+ Limeneli ndi gawo lawo lochokera pansembe zowotcha pamoto+ zoperekedwa kwa Yehova, mʼmibadwo yanu yonse mpaka kalekale. Chilichonse chimene chingakhudze nsembezi chidzakhala choyera.’”
18 Mwamuna aliyense mwa ana a Aroni azidya mkatewo.+ Limeneli ndi gawo lawo lochokera pansembe zowotcha pamoto+ zoperekedwa kwa Yehova, mʼmibadwo yanu yonse mpaka kalekale. Chilichonse chimene chingakhudze nsembezi chidzakhala choyera.’”