Levitiko 7:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Nyama ya nsembe yakupalamula aziiphera pamalo amene amaphera nyama ya nsembe yopsereza, ndipo magazi ake+ aziwazidwa mbali zonse za guwa lansembe.+
2 Nyama ya nsembe yakupalamula aziiphera pamalo amene amaphera nyama ya nsembe yopsereza, ndipo magazi ake+ aziwazidwa mbali zonse za guwa lansembe.+