Levitiko 7:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Wansembe aziwotcha zinthu zimenezi paguwa lansembe monga nsembe yowotcha pamoto yoperekedwa kwa Yehova.+ Imeneyi ndi nsembe yakupalamula.
5 Wansembe aziwotcha zinthu zimenezi paguwa lansembe monga nsembe yowotcha pamoto yoperekedwa kwa Yehova.+ Imeneyi ndi nsembe yakupalamula.