Levitiko 7:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Lamulo la nsembe yakupalamula ndi lofanana ndi la nsembe yamachimo. Nyama ya nsembeyi izikhala ya wansembe amene wapereka nsembeyo pophimba machimo.+
7 Lamulo la nsembe yakupalamula ndi lofanana ndi la nsembe yamachimo. Nyama ya nsembeyi izikhala ya wansembe amene wapereka nsembeyo pophimba machimo.+