Levitiko 7:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Wansembe akaperekera munthu nsembe yopsereza, chikopa+ cha nsembeyo chizikhala cha wansembe amene wapereka nsembeyo.
8 Wansembe akaperekera munthu nsembe yopsereza, chikopa+ cha nsembeyo chizikhala cha wansembe amene wapereka nsembeyo.