-
Levitiko 7:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Azipereka nsembe yake pamodzi ndi mitanda ya mkate yozungulira yoboola pakati, yokhala ndi zofufumitsa. Aziipereka pamodzi ndi nsembe zamgwirizano zimene akuzipereka posonyeza kuyamikira.
-