Levitiko 7:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Koma ngati nyama ya nsembeyo yatsala mpaka tsiku lachitatu, ayenera kuiwotcha pamoto.+