18 Koma ngati nyama iliyonse ya nsembe yamgwirizano yadyedwa pa tsiku lachitatu, wopereka nsembeyo Mulungu sadzasangalala naye. Nsembe yakeyo idzakhala yopanda phindu. Idzakhala chinthu chonyansa, ndipo amene wadya nsembeyo adzayankha mlandu chifukwa cha kulakwa kwake.+