-
Levitiko 7:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Nyama imene yakhudza chilichonse chodetsedwa, siyenera kudyedwa. Muziiwotcha pamoto. Koma aliyense woyera angathe kudya nyama imene sinadetsedwe.
-