Levitiko 7:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Mafuta a nyama imene mwaipeza yakufa komanso mafuta a nyama imene yaphedwa ndi nyama inzake, mungathe kuwagwiritsa ntchito iliyonse, koma musamawadye ngakhale pangʼono.+
24 Mafuta a nyama imene mwaipeza yakufa komanso mafuta a nyama imene yaphedwa ndi nyama inzake, mungathe kuwagwiritsa ntchito iliyonse, koma musamawadye ngakhale pangʼono.+