Levitiko 7:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Musamadye magazi alionse+ kulikonse kumene mungakhale, kaya akhale magazi a mbalame kapena a nyama.
26 Musamadye magazi alionse+ kulikonse kumene mungakhale, kaya akhale magazi a mbalame kapena a nyama.