Levitiko 7:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Wansembe aziwotcha mafutawo paguwa lansembe,+ koma chidalecho chizikhala cha Aroni ndi ana ake.+