Levitiko 7:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Yehova analamula kuti aziwapatsa gawoli kuchokera kwa Aisiraeli, pa tsiku limene anawadzoza.+ Limeneli ndi lamulo mʼmibadwo yawo yonse mpaka kalekale.’”
36 Yehova analamula kuti aziwapatsa gawoli kuchokera kwa Aisiraeli, pa tsiku limene anawadzoza.+ Limeneli ndi lamulo mʼmibadwo yawo yonse mpaka kalekale.’”