Levitiko 7:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Limeneli ndi lamulo lokhudza nsembe yopsereza,+ nsembe yambewu,+ nsembe yamachimo,+ nsembe yakupalamula,+ nyama yoperekedwa poika munthu kuti akhale wansembe+ ndiponso nsembe yamgwirizano,+
37 Limeneli ndi lamulo lokhudza nsembe yopsereza,+ nsembe yambewu,+ nsembe yamachimo,+ nsembe yakupalamula,+ nyama yoperekedwa poika munthu kuti akhale wansembe+ ndiponso nsembe yamgwirizano,+