Levitiko 7:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 mogwirizana ndi zimene Yehova analamula Mose paphiri la Sinai,+ pa tsiku limene analamula Aisiraeli kuti azipereka nsembe zawo kwa Yehova mʼchipululu cha Sinai.+
38 mogwirizana ndi zimene Yehova analamula Mose paphiri la Sinai,+ pa tsiku limene analamula Aisiraeli kuti azipereka nsembe zawo kwa Yehova mʼchipululu cha Sinai.+