Levitiko 8:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Kenako Mose anaitana ana a Aroni nʼkuwapaka magazi mʼmunsi pakhutu lawo lakumanja, pachala chawo chamanthu kudzanja lamanja ndi pachala chawo chachikulu cha mwendo wakumanja. Koma magazi otsalawo, Mose anawawaza mbali zonse za guwa lansembe.+ Levitiko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:24 Nsanja ya Olonda,11/15/2014, ptsa. 9-10
24 Kenako Mose anaitana ana a Aroni nʼkuwapaka magazi mʼmunsi pakhutu lawo lakumanja, pachala chawo chamanthu kudzanja lamanja ndi pachala chawo chachikulu cha mwendo wakumanja. Koma magazi otsalawo, Mose anawawaza mbali zonse za guwa lansembe.+